2 Mafumu 21:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo sindidzacotsanso mapazi a Israyeli m'dziko ndidalipereka kwa makolo ao; cokhaci asamalire kucita monga mwa zonse ndawalamulira ndi monga mwa cilamulo conse anawalamulira Mose mtumiki wanga.

2 Mafumu 21

2 Mafumu 21:1-16