2 Mafumu 20:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndakuonjezera pa masiku ako zaka khumi ndi zisanu; ndidzakupulumutsa iwe ndi mudzi uno m'dzanja la mfumu ya Asuri; ndidzacinjiriza mudzi uno, cifukwa ca Ine ndekha, ndi cifukwa ca Davide mtumiki wanga.

2 Mafumu 20

2 Mafumu 20:3-16