2 Mafumu 2:24-25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

24. Ndipo anaceuka, nawaona, nawatemberera m'dzina la Yehova. Ndipo kuthengo kunaturuka zimbalangondo ziwiri zazikazi, ndi kupwetedza mwa iwo ana makumi anai mphambu awiri.

25. Ndipo anacokako kumka ku phiri la Karimeh; nabwera kumeneko nafika ku Samariya.

2 Mafumu 2