2 Mafumu 19:37 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipokunali popembedza iye m'nyumba ya Nisiroki mulungu wace, Adrameleki ndi Sarezere anamkantha ndi lupanga; napulumukira ku dziko la Ararati. Ndipo Esarihadoni mwana wace anakhala mfumu m'malo mwace.

2 Mafumu 19

2 Mafumu 19:30-37