2 Mafumu 19:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cherani khutu lanu, Yehova, nimumve; tsegulani maso anu, Yehova, nimupenye; ndipo imvani mau a Sanakeribu, amene anatumiza kutonza nao Mulungu wamoyo.

2 Mafumu 19

2 Mafumu 19:6-26