2 Mafumu 18:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iri kuti milungu ya Hamati, ndi ya Aripadi? iri kuti milungu ya Sefaravaimu, kapena Hena, ndi Iva? Kodi yalanditsa Samariya m'dzanja langa?

2 Mafumu 18

2 Mafumu 18:25-37