2 Mafumu 18:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Naima kazembeyo, napfuula ndi mau akulu m'Ciyuda, nanena kuti, Tamverani mau a mfumu yaikuru mfumu ya Asuri.

2 Mafumu 18

2 Mafumu 18:23-35