2 Mafumu 17:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Caka cakhumi ndi ziwiri ca Ahazi mfumu ya Yuda Hoseya mwana wa Ela analowa ufumu wace wa Israyeli m'Samariya, nakhala mfumu zaka zisanu ndi zinai.

2. Nacita iye coipa pamaso pa Yehova, koma osati monga mafumu a Israyeli asanakhale iye.

2 Mafumu 17