2 Mafumu 13:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Caka ca makumi awiri ndi zitatu ca Yoasi mwana wa Ahaziya mfumu ya Yuda, Yoahazimwana wa Yehu analowa ufumu wace wa Israyeli ku Samariya, nakhala mfumu zaka khumi ndi zisanu ndi ziwiri.

2 Mafumu 13

2 Mafumu 13:1-5