2 Mafumu 11:20-21 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Nakondwerera anthu onse a m'dziko, ndi m'mudzi munali phe; ndipo adapha Ataliya ndi lupanga ku nyumba ya mfumu.