2 Akorinto 9:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ndatuma abale kuti kudzitamandira kwathu kwa pa inu kusakhale kopanda pace m'menemo; kuti, monga ndinanena, mukakhale okonzekeratu;

2 Akorinto 9

2 Akorinto 9:1-9