2 Akorinto 2:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Koma ndinatsimikiza mtima mwa ine ndekha, ndisadzenso kwa inu ndi cisoni.

2. Pakuti ngati ine ndimvetsa inu cisoni, ndaninso amene adzandikondweretsa ine, kama iye amene ndammvetsa cisoni?

2 Akorinto 2