2 Akorinto 13:11-14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

11. Cotsalira, abale, kondwerani, Mucitidwe angwiro; mutorithozedwe; khalani a mtima umodzi, khalani mumtendere; ndipo Mulungu wa cikondi ndi mtendere akhale pamodzi ndi inu.

12. Lankhulanani ndi cipsompsono copatulika.

13. Oyera mtima onse alankhula inu,

14. Cisomo ca Ambuye Yesu Kristu, ndi cikondi ca Mulungu, ndi ciyanjano ca Mzimu Woyera zikhale ndi inu nonse.

2 Akorinto 13