2 Akorinto 10:16-18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

16. kukalalikira Uthenga Wabwino m'tsogolo mwace mwa inu, sikudzitamandira mwa cilekezero ca wina, ndi zinthu zokonzeka kale.

17. Koma iye wodzitamandira adzitamandire mwa Ambuye;

18. pakuti si iye amene adzitama yekha, koma iye amene Ambuye amtama ali wobvomerezeka.

2 Akorinto 10