2 Akorinto 1:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti sitifuna abale, kuti mukhale osadziwa za cisautso cathu tinakomana naco m'Asiya, kuti tinathodwa kwakukuru, koposa mphamvu yathu, kotero kuti tinada nkhawa ngakhale za moyo wathu;

2 Akorinto 1

2 Akorinto 1:2-15