2 Akorinto 1:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

woo titonthoza ife m'nsautso yathu yonse, kuti tidzathe ife kutonthoza iwo okhala m'nsautso iri yonse, mwa citonthozo cimene titonthozedwa naco tokha ndi Mulungu.

2 Akorinto 1

2 Akorinto 1:1-7