2 Akorinto 1:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti Mwana wa Mulungu, Yesu Kristu, amene analalikidwa mwa inu ndi ife, (ine ndi Silvano ndi Timoteo) sanakhala eya ndi iai, koma anakhala eya mwa iye.

2 Akorinto 1

2 Akorinto 1:12-24