2 Akorinto 1:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo, pakufuna cimene, kodi ndinacitapo kosinthasintha? Kapena zimene nditsimikiza mtima kodi ndizitsimikiza mtima monga mwa thupi? Kuti pa ine pakhale eya, eya, ndi iai, iai?

2 Akorinto 1

2 Akorinto 1:16-24