1 Samueli 30:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndani adzabvomerezana nanu mrandu uwu? Pakuti monga gawo lace la iye wakumuka kunkhondoko, momwemo lidzakhala gawo lace la iye wakukhala ndi akatundu, adzagawana cimodzimodzi.

1 Samueli 30

1 Samueli 30:18-31