1 Samueli 14:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Sauli ndi anthu onse amene anali naye anaunjikana pamodzi, naturukira kunkhondoko; ndipo taonani, munthu yense anakantha mnzace ndi lupanga, ndipo panali kusokonezeka kwakukuru.

1 Samueli 14

1 Samueli 14:17-24