1 Samueli 12:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace tsono, imani pano, kuti ndiweruzane nanu pamaso pa Yehova za nchito zonse zolungama za Yehova, anakucitirani inu ndi makolo anu.

1 Samueli 12

1 Samueli 12:1-8