1 Samueli 10:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mbale wa atate wace wa Sauli ananena kwa iye ndi mnyamata wace, Munanka kuti? Ndipo iye anati, Kukafuna aburuwo; ndipo pakuona kuti sitinawapeza, tinadza kwa Samueli.

1 Samueli 10

1 Samueli 10:10-15