1 Petro 4:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa yafika nthawi kuti ciweruziro ciyambe pa nyumba ya Mulungu; komangati ciyamba ndi ife, citsiriziro ca iwo osamvera Uthenga Wabwino wa Mulungu cidzakhala ciani?

1 Petro 4

1 Petro 4:8-19