1 Petro 2:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma inu ndinu mbadwa yosankhika, ansembe acifumu, mtundu woyera mtima, anthu a mw ni wace, kotero kuti mukalakire zoposazo za iye amene anakuitanani muturuke mumdima, mulowe kuunika kwace kodabwitsa;

1 Petro 2

1 Petro 2:2-17