1 Mbiri 8:20-22 Buku Lopatulika 1992 (BL92) ndi Elianai, ndi Ziletai, ndi Elieli, ndi Adaya, ndi Beraya, ndi Simirati, ana a Simei; ndi Isipani, ndi Eberi