14. ndi Ahio, Sasaki, ndi Yeremoti,
15. ndi Zebadiya, ndi Aradi, ndi Ederi,
16. ndi Mikaeli, ndi Isipa, ndi Yoha, ana a Beriya;
17. ndi Zebadiya, ndi Mesulamu, ndi Hiziki, ndi Heberi,
18. ndi Ismerai, ndi Izliya, ndi Yobabu, ana a Elipaala;
19. ndi Yakimu, ndi Zikiri, ndi Zabidi,
20. ndi Elianai, ndi Ziletai, ndi Elieli,
21. ndi Adaya, ndi Beraya, ndi Simirati, ana a Simei;