1 Mbiri 8:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo Benjamini anabala Bela mwana wace vyoyamba, Asibeli waciwiri, ndi Ahara wacitatu,

2. Noha wacinai, ndi Rafa wacisanu.

3. Ndi Bela anali ndi ana: Adara, ndi Gera, ndi Abihudi,

1 Mbiri 8