1 Mbiri 6:8-11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

8. ndi Ahitubu anabala Zadoki, ndi Zadoki anabala Ahimaazi,

9. ndi Ahimaazi anabala Azariya, ndi Azariya anabala Yohanani,

10. ndi Yohanani anabala Azariya (ndiye amene anacita nchito ya nsembe m'nyumba anaimanga Solomo m'Yerusalemu),

11. ndi Azariya anabala Amariya, ndi Amariya anabala Ahitubu,

1 Mbiri 6