1 Mbiri 6:5-8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

5. ndi Abisua anabala Buki, ndi Buki anabala Uzi,

6. ndi Uzi anabala Zerahiya, ndi Zerahiya anabala Merayoti,

7. Merayoti anabala Amariya, ndi Amariya anabala Ahitubu,

8. ndi Ahitubu anabala Zadoki, ndi Zadoki anabala Ahimaazi,

1 Mbiri 6