1 Mbiri 6:16-18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

16. Ana a Levi: Gerisomu, Kohati ndi Merari.

17. Ndipo maina a ana a Gerisomu ndi awa: Libni, ndi Simei.

18. Ndipo ana a Kohati ndiwo Amramu, ndi lzara, ndi Hebroni, ndi Uzieli.

1 Mbiri 6