1 Mbiri 4:42-43 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

42. Ndipo ena a iwowa a ana a Simeoni, amuna mazana asanu, anamka ku phiri la Seiri; akuwatsogolera ndiwo Pelatiya, ndi Neariya, ndi Refaya, ndi Uzieli; ana a lsi.

43. Nakantha otsala a Aamaleki adapulumukawo, nakhala komweko mpaka lero lino.

1 Mbiri 4