1 Mbiri 3:17-22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

17. Ndi mwana wa Yekoniya: Asiri, Sealitiyeli mwana wace,

18. ndi Malikiramu, ndi Pedaya, ndi Senazara, Yekamiya, Hosama, Nedabiya.

19. Ndi ana a Pedaya: Zerubabeli, ndi Simei; ndi ana a Zerubabeli: Mesulamu, ndi Hananiya; ndipo Selomiti ndiye mlongo wao,

20. ndi Hasuba, ndi Oheli, ndi Berekiya, ndi Hasadiya, ndi Yusabi-hesedi; asanu.

21. Ndi ana a Hananiya: Pelatiya, ndi Yesaya, ana a Refaya, ana a Arinani, ana a Obadiya, ana a Sekaniya.

22. Ndi mwana wa Sekaniya: Semaya; ndi ana a Semaya: Hatusi, ndi Igali, ndi Bariya, ndi Neariya, ndi Safati; asanu ndi mmodzi.

1 Mbiri 3