1 Mbiri 3:15-20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

15. Ndi ana a Yosiya: woyamba Yohanana, waciwiri Yehoyakimu, wacitatu Zedekiya, wacinai Salumu.

16. Ndi ana a Yehoyakimu: Yekoniya mwana wace, Zedekiya mwana wace.

17. Ndi mwana wa Yekoniya: Asiri, Sealitiyeli mwana wace,

18. ndi Malikiramu, ndi Pedaya, ndi Senazara, Yekamiya, Hosama, Nedabiya.

19. Ndi ana a Pedaya: Zerubabeli, ndi Simei; ndi ana a Zerubabeli: Mesulamu, ndi Hananiya; ndipo Selomiti ndiye mlongo wao,

20. ndi Hasuba, ndi Oheli, ndi Berekiya, ndi Hasadiya, ndi Yusabi-hesedi; asanu.

1 Mbiri 3