1 Mbiri 29:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mfumu Davide ananenanso kwa khamu lonse, Mulungu wasankha mwana wanga Solomo yekha, ndiye mnyamata ndi wosakhwima; ndipo nchitoyi ndi yaikuru, pakuti cinyumbaci siciri ca munthu, koma ca Yehova Mulungu.

1 Mbiri 29

1 Mbiri 29:1-3