1 Mbiri 23:16-20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

16. Ana a Gerisomu: wamkuru ndi Sebuyeli.

17. Ndi ana a Eliezeri: wamkuru ndi Rehabiya. Ndipo Eliezeri analibe ana ena, koma ana a Rehabiya anacuruka kwambiri.

18. Ana a Izara: wamkuru ndiye Selomiti.

19. Ana a Hebroni: wamkuru ndi Yeriya, waciwiri ndi Amariya, wacitatu ndi Yehazieli, wacinai ndi Yekameamu,

20. Ana a Uzieli: wamkuru ndi Mika, waciwiri ndi Isiya.

1 Mbiri 23