1 Mbiri 19:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene ana a Amoni anaona kuti anadzinunkhitsa kwa Davide, Hanuni ndi ana a Amoni anatumiza matalente cikwi cimodzi a siliva, kudzilembera magareta ndi apakavalo ku Mesopotamiya, ndi ku Aramu-maaka, ndi ku Zoba.

1 Mbiri 19

1 Mbiri 19:1-16