1 Mbiri 15:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Alevi anaika Hemani mwana wa Yoeli, ndi a abale ace Asafu mwana wa Berekiya, ndi a ana a Merari, abale ao, Etani mwana wa Kusaya;

1 Mbiri 15

1 Mbiri 15:15-22