1 Mbiri 11:43-47 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

43. Hanani mwana wa Maaka, ndi Yosafati Mmitini,

44. Uziya M-asterati, Sama ndi Yeieli ana a Hotamu wa ku Aroeri,

45. Yedyaeli mwana wa Simri, ndi Yoha mbale wace Mtizi,

46. Elieli Mmahavi, ndi Yeribai ndi Yosaviya ana a Elinaamu, ndi Itima Mmoabu,

47. Elieli, ndi Obedi, ndi Yasiyeli Mmezobai.

1 Mbiri 11