1 Mbiri 1:27-31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

27. Abramu, (ndiye Abrahamu).

28. Ana a Abrahamu: Isake, ndi Ismayeli.

29. Mibadwo yao ndi awa; woyamba wa Ismayeli Nebayoti; ndi Kedara ndi Adibeli, ndi Mibisamu,

30. Misma, ndi Duma Masa,

31. Hadada, ndi Tema, Nafisi, ndi Kedema. Awa ndi ana a Ismayeli.

1 Mbiri 1