1 Mbiri 1:21-32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

21. ndi Hadoramu, ndi Uzali, ndi Dikila;

22. ndi Ebala, ndi Abimaele, ndi Seba,

23. ndi Ofiri, ndi Havila, ndi Yobabi. Awa onse ndiwo ana a Yokitani.

24. Semu, Aripakisadi, Sela;

25. Eberi, Pelegi, Reu,

26. Serugi, Nahori, Tera;

27. Abramu, (ndiye Abrahamu).

28. Ana a Abrahamu: Isake, ndi Ismayeli.

29. Mibadwo yao ndi awa; woyamba wa Ismayeli Nebayoti; ndi Kedara ndi Adibeli, ndi Mibisamu,

30. Misma, ndi Duma Masa,

31. Hadada, ndi Tema, Nafisi, ndi Kedema. Awa ndi ana a Ismayeli.

32. Ndi ana a Ketura mkazi wamng'ono wa Abrahamu anabala Zimiramu, ndi Yokisani, ndi Medani, ndi Midyani, ndi Isibaki, ndi Sua. Ndi ana a Yokisani: Seba, ndi Dedani.

1 Mbiri 1