1 Mbiri 1:15-20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

15. ndi Ahivi, ndi Aariki, ndi Asini,

16. ndi Aarivadi, ndi Azemari, ndi Ahamati.

17. Ana a Semu: Elamu, ndi Asuri, ndi Aripakisadi, ndi Ludi, ndi Aramu, ndi Uzi, ndi Huli, ndi Geteri, ndi Meseki.

18. Ndi Aripakisadi anabala Sela; ndi Sela anabala Eberi.

19. Ndi Eberi anabala ana amuna awiri, dzina la winayo ndiye Pelegi, popeza masiku ace dziko linagawanika; ndi dzina la mbale wace ndiye Yokitani.

20. Ndipo Yokitani anabala Almodadi, ndi Selefi, ndi Hazaramaveti, ndi Yera;

1 Mbiri 1