1 Mafumu 9:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anati kwa iye, Ndamva pemphero lako ndi pembedzero lako wandipembedza nalo; ndapatula nyumba imene waimangayi kuikamo dzina langa nthawi zosatha, ndipo maso anga ndi mtima wanga zidzakhala kumeneko masiku onse.

1 Mafumu 9

1 Mafumu 9:1-12