1 Mafumu 7:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anaimiritsa nsanamirazi pa likole la Kacisi; naimiritsa nsanamira ya ku dzanja lamanja, nacha dzina lace Yakini; naimiritsa nsanamira yakumanzere, nacha dzina lace Boazi.

1 Mafumu 7

1 Mafumu 7:19-25