1 Mafumu 5:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Hiramu anatumiza kwa Solomo, nati, Ndazimva zija munatumiza kwa inezo, ndidzacita cifuniro canu conse, kunena za mitengo yamkungudza ndi mitengo yamlombwa.

1 Mafumu 5

1 Mafumu 5:1-11