1 Mafumu 20:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mudziwerengere khamu la nkhondo longa khamu lija lidaonongekalo, ndi akavalo onga akavalo aja, ndi magareta monga omwe aja; ndipo tikaponyane nao pacidikha tidzawapambana ndithu. Namvera iye mau ao, natero kumene.

1 Mafumu 20

1 Mafumu 20:22-32