1 Mafumu 17:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mbiya ya ufa siidatha, ndi nsupa ya mafuta siinacepa, monga mwa mau a Yehova amene ananenetsa Eliya.

1 Mafumu 17

1 Mafumu 17:10-18