1 Mafumu 14:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo ndinalanda nyumba ya Davide ufumu, ndi kuupereka kwa iwe, koma sunafanana ndi Davide mtumiki wanga uja, amene anasunga malamulo anga, nanditsata ndi mtima wace wonse kucita zolunjika zokha zokha pamaso panga;

1 Mafumu 14

1 Mafumu 14:1-12