1 Mafumu 14:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo masiku akukhala Yerobiamu mfumu anali zaka makumi awiri mphambu ziwiri, nagona iye kwa makolo ace, nalowa ufumu m'malo mwace Nadabu mwana wace.

1 Mafumu 14

1 Mafumu 14:12-26