1 Mafumu 11:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma sindidzalanda ufumu wonse m'dzanja lace, koma ndidzamkhalitsa mfumu masiku ace onse, cifukwa ca Davide mtumiki wanga amene uja ndinamsankha, cifukwa kuti anasunga malamulo anga ndi malemba anga.

1 Mafumu 11

1 Mafumu 11:33-41