1 Mafumu 1:44 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo mfumu yatumanso Zadoki wansembe, ndi Natani mneneri, ndi Benaya mwana wa Yehoyada, ndi Akereti, ndi Apeleti aja, namkweza iye pa nyuru ya mfumu.

1 Mafumu 1

1 Mafumu 1:37-47